Intro
Mmmmmm yeah yeah yeah yeah
Khanga boy
Mablaza music to the nation
Verse 1
Ndikufuna mtima wako or anakuswera
Sindilota wina ndiwe mtima unandibera
Ndadziyika myself above you
Not to be a master koma be your shield
Come to my bed undivetse kukoma
I can't spend a day without think about u
Ndakukonda ndine kuti ukhale waine
Ngati alipo anakusiya ayiwale zaiwe
Usiku mkamagona ndimalota zaiwe
Kuti moyo wanga wonse udzakhale waine
No matter the distance ndili naiwe
Palibe adzakulize ngati uli naine
Hook
Ngati zokoma ndizotere
Your my forever story
Zakale zapita ndi history
Alhamdulilah poti mwatere
Yeah yeah eee
look at smile.. nobody!
look at style.. nobody!
look at face.. nobody!
Until forever.. nobody!
Verse2
Pano love ili stable stable
Ndatola kanga ka memo stable
Kangotengera amake Kali ndendende
Lero tichezera mpaka mbembembe
Ndipatse mtima wako undivetsetse
Yemwe anakusiya azelezeke
Ma hope ndi ma x tiwadulile malire
I wish to God ndikukwatile
Zomacheza kumawopa akwanu zatha
Zondivomela kumbari kumandikana zatha
Kako Kako kamafuna kuchengetela
Sendera pafupi mwana kazi mwetulila
Ine pa iwe wekha I pray to God
Opanga ma jealous kuti adzipepela
Bridge
Koma ngati dzapita kumanda
Ukulumbila udzanditsata aaa
Koma ngati dzapita kukaya
Ukulumbila sudzapezaso winaa
Hook
Ngati zokoma ndizotere
Your my forever story
Zakale zapita ndi history
Alhamdulilah poti mwatere
Yeah yeah eee
look at smile.. nobody!
look at style.. nobody!
look at face.. nobody!
Until forever.. nobody!
Ending
Mablaza music to the nation