Mmmh mmm anuchi fire works music.
Yeaaa.
Peter bandah!!
Hello, mmh hello! bwenzi langa.
moyo waku world simkuziwa ulibwanji.
Chimalizire sukulu mix sitinakumane.
Inee anuchi zikundivuta.
Kukhala opanda iwe mkukanika mmh.
Ndikumakusowaaa aa.
Ndikufuna iweyo ooohh.
Ndikakumbukila mene umandisekelera.
Sindikufuna wina mamie nakuzolowera.
Pena ndikakhala nkhawa ikumazandigwira.
Tinakumana lija ndikale ine manthaa mm manthaa.
"Utha kupeza wina mkundisiya"
Anga ndimatha ineeeeeeee aaaaaaahhh manthaaa.
Long distance isatipange influence.
Tisalole ubale wanthu itipange separate.
Maweeeeee eeeee mmmmmm mmm eee.
" Anuchi peter banda aaaaah"
Singakwaniseeee ineyoooo oooh mmmh.
Chirus;
Hello my love, how are you.
Ine singakwanise khala opanda you.
I miss you mmmm mamiweeee.
When will i Meet you mmh.
Ndisaname ndikumakusowa.
Kukhala opanda iww life yanga ikubowa.
Koma bwanji tikumane eeeh.
Pali nkhani tikambilane eeee.
Ndikakhala pansi za iwe ndizomwe ndimalabadira.
Kuzakhala nawe chifupi moyo mwanga ndizomwe ndimakhumbila ine mmmh.
Bridge;
Uuuuh mmmmm
" Anuchi fire works music"
Peter banda production,
Mmmhhhh mmmh aaaa
Ndufuna iweyoooo aaaaa
Iweyoooo mmmmh ..
Ndikumakusowa iweeeee.
Ndiwe moyo wanga wanga ineeeeee.
You are my every thing"