[Intro]
[Verse 1]
Pachimbi Mulungu adalenga dziko,
Dziko lokhala ndi kuwala
Dziko lokhala ndi dima, lokhala ndi zokoma ndi zowawa, lokhala ndi thawi ndi yokondwera ndi nyengo yosithasitha
Adalenganso anthu osiyana machitidwe chokhalidwe,maonekedwe ndi kaganizidwe
[Bridge]
koma ndalira popeza Mulungu adalenga zinsinsi.
Kusekerera kwa muntu kuoneka m'milomo m'kati muli khondo.
Ndalira, ndalira popezaaa!!!
[Chorus]
leader: ndinadziwe,
choir: sindinadziwe,
leader: sindinadziwe choir: sindinadziwe
(All together):
Kuti khope ya munthu ibisa zambiri
Amakumwetulira, amakunyadira pa leader: pamanso
Leader: Mumtima muli misapha,
Choir: acheza nawe,
Avina nawe kumbari leader: akumemeza khondo .
Choir: Sindinadziwe, Sindinadziwe, Sindinadziwe. Leader: inee!!
[Verse 2]
Osakhulupirira maonekedwe a khope ya okondedwa was pa dziko amakhumudwitsa.
Khulupirira Yehova yekha.
Iye sdzakhala bwezi lako lokhulupirika.
Mu nthawi zooonse.
Amen.
[Bridge]
-

[Outro]
Osakhulupirira maonekedwe a khope ya okondedwa was pa dziko amakhumudwitsa.
Khulupirira Yehova yekha.
Iye sdzakhala bwezi lako lokhulupirika.
Mu nthawi zooonse.
Amen.