[Intro]
Oyah oyah, yahh mhmh
Yes of course, ndi dziyamikile ndekha
Kuti ndifike pomwe. Ndilipa sizinali zophweka
Mr.emtee kachikena
Tickets beats
[Chorus]
That's okay
That's alright
Go ahead
Leave life
[Verse 1]
Dziwa dima. umadana ndi Toch
Pali awili. pamakhala kochi
Chikond Chikatha. zimakhala chonchi
Koma may. mukadapola moto
Pakuti Chikond. Ndi mathelo ankhondo
ntchimo lili lonse. lili nayo yake mphoto
Chikond chikatha umadza ndi udan
Kodi iwe ndine adalakwitsa. Ndan
Basi tidzawonana may endaniii..
[Chorus]
that's okay,
that's alright [x2]
mr. Patrick ase
[Verse 2]
nzowonad may. pitan,
kwakwana. ndakupililan,
pamaso panga. chokan,
kwinako ndiwona. kut nditan,
Chikond changa chaku.kanikan,
atakhala mwanay,
akakhala nda may,
bas may bye bye
[Chorus]
That's okay,
that's alright,
Go ahead,
Leave life,[x2]
[Verse 3]
Chikond chanji choyendela season,
Chomangoyambana opanda ma reason,
There is no reason to love,
But it's ok. am so fine,
Yendan may tidza. wonana,
Nzo
[Outro]
Chikond chikatha, utalandira chimodzi, tisankhane
Ndikhoza kukumbukira ndekha, kupita patsogolo
That’s okay, that’s alright, tikhale chete