[Intro]
Yeah, Bashiluh Malawi, MPHWIZA on the track
[Verse 1]
Moyo ndiwovuta, mukazitengela za life, ndizovuta
Zokhumba zamoyo ndizambili, ine ndinali mozi mwa ozitengera zah life pano
Ndine ndikupanga regret, of course sindine wa zama love, chifukwa love is blind
[Chorus]
Moyo moyo ndiwovuta, moyo moyo ndiwovuta, iiiih aaaah
Moyo moyo ndiwovuta, moyo moyo ndiwovuta, iiiih aaaah
[Verse 2]
Yeah, it's Bashiluh you know, pano ndikukhala moyo okonda abale ndi ndalama
Zokhumba zamoyo sizikwana kuwutengela moyo, ukhoza kupenga
Ndiyes bola just be cool in life, but sometimes it needs to be angry man with money
Not gossip, people life ndiyovuta, eeeeeh! oooooh!
Yeah it's Bashiluh Malawi, yeah hmmm yeah yeah yeah MPHWIZA Malawi, our own producer
Yeah (Goatso's on the track!)
[Chorus]
Moyo moyo ndiwovuta, moyo moyo ndiwovuta, iiiih aaaah
Moyo moyo ndiwovuta, moyo moyo ndiwovuta, iiiih aaaah
[Bridge]
Kukula kwa moyo, kulambira pa mtima, mwachikondi kapena mwakhumba
Zinthu za moyo zimasanda, palibe chomwe chimatiuza
[Chorus]
Moyo moyo ndiwovuta, moyo moyo ndiwovuta, iiiih aaaah
Moyo moyo ndiwovuta, moyo moyo ndiwovuta, iiiih aaaah
[Outro]
Goatso's on the track, Tanzania to Malawi, tsopano ndi tsopano, ndili pano