Verse 1
Tinayamba ndi loto, ndi tiyi pang’ono ☕
Takhala mozungulira ngati banja limodzi
Nestone anati, “Tisinthe dziko lero!”
Koma choyamba… ndani anayiwala mpunga? 😅
Pre-Chorus
Dyangale “Khalani oleza mtima!” Dailes “Relax basi!”
Woza anabweretsa samosa, tonse “Bismillah!” basi 😄
Chorus
🌙 FULL MOOOON, timawala usiku!
Tikuchita zabwino, kufuna kuchita bwino!
Tikuseka limodzi, kupemphera molimbika,
Ngakhale foni ya Abada ikulira nthawi ya swala! 📱😂
🌙 FULL MOOOON, tikukwera mmwamba!
Kuthandiza anthu, kufika kumadulira!
Ukabweretsa chakudya, amakukonda kwambiri…
(Koma ukabwera opanda… amakukondabe chifukwa cha Jolobala anawandikira manda 😇)
Verse 2
Tinapita kwasafali, tili ndi mphamvu 🌳
Koma tisanathe… zinthu zinasintha
“Ndani wabweretsa madzi?” — chete basi, Yasinta ndi Shakira akugula thobwa 🤐
Tsopano tamvesera, Abu Badriya Sakhala kwa Safali😭
Komabe kwasafali mkovaya. Kwazaza madolo
Pre-Chorus
Katete anati “Khalani serious!” tinati “Zili bwino!” koma Achi phokoso, mpaka Shina watuluka
Koma patapita mphindi 5… anayamba kusokonezanso 😅
Hahahaha koma Koma Dyangale
Chorus
🌙 FULL MOOOON, timawala usiku!
Nthawi zina serious… nthawi zina osangalala!
Kupanga ma poster, kukhala bwino,
Kenako wina “Eish… mawu ena wasiya!” 😭😂
🌙 FULL MOOOON, sitimataya mtima!
Ngakhale tiyambane, sitikwiya ☕
Kugwira ntchito limodzi, mokondana,
Ngakhale ma meeting amasanduka masewera a chakudya 😆
Bridge (Yochepa, yoseketsa)
Ohhhh… ndani watenga pen yanga? 🖊️
Ndani wasuntha mpando?
Ndani wadya samosa wa Zuga… vomerezani tsopano kuti Yasin amadya kwambili 👀😂
Final Chorus
🌙 FULL MOOOON, ndife amozi!
Sitikwanira, koma tikuyesetsa!
Ndi chikhulupiriro champhamvu ndi mtima wowala,
Tipitiliza kuwala ngati mwezi usiku 🌙✨
🎤 Outro:
“Meeting mawa?”
“InshaAllah!”
“Bweretsani chakudya?”
“INSHAAAALLAAAH!” 😂😂
Osaiwala phala KING!