* KHAI CEE - MY LOVER RECHO*
*[CHORUS - KHAI CEE - Softer Voice - Sweet]*
A Kay zm featuring Khai cee My lover Recho( Recho) nikondeko
Baby ukhale mai wawana wanga
Cifukwa mu umayo wanga uli chalo
Chango paka ifa so baby Recho
Nikonde ndiwe mai wanga nipase love
Na thupi yako yokondwelesa makolo
Anga kuti niimbe nyimbo nilifa cifukwa
Tulo twamala niganiza iwe my lover
Wanga paka ifa ndipe nthawi zonse
Nilota iwe ngakhale mudzuwa kapena usiku
*[RAP x2 - Traditional Rap Style - Bass Voice - Deep]*
Recho uli mai wanga kulibe wamene
Angatenge mutima uyu cifukwa iwe
Ndiwe unasiliza space( space) nikonda
Iwe basiiii kwa(kwa)( kwa) sila so
Nikonde weeeeeeh oooooh maiiiih
Wandi kapena sweetiiii h Wandiii
(Wandi)( Wandi)Sweetiiih)(Sweetiiih)
*[CHORUS - Repeat - Softer Voice + Dancer - 2x]*
My lover Recho(Recho) nikondeko
Baby ukhale mai wakwana wanga
Cifukwa mu umayo wanga uli chalo
Chango paka ifa so baby Recho
Nikonde ndiwe mai wanga nipase love
Na thupi yako yokondwelesa makolo
Anga kuti niimbe nyimbo nilifa cifukwa
Tulo twamala niganiza iwe my lover
Wanga paka ifa ndipo nthawi zonse
Nilota iwe ngakhale mudzuwa kapena usiku
*[RAP - Repeat - Different Voice - Bass + Echo]*
Recho uli mai wanga kulibe wamene
Angatenge mutima uyu cifukwa iwe
Ndiwe unasiliza space(space) nikonda iwe
Basiiii kwa,( kwa), (kwa), sila so nikonde
Weeeeeeh oooooh maiiiih Wandi
Kapena sweetiiiih Wandiii
(Wandi), (Wandi), Sweetiiih,( Sweetiiih)
*[OUTRO - Softer Voice - Whisper]*
_Recho... my lover... Recho..._
_Nikondeko... baby... usiku na mudzuwa..._
_Recho... Wandi... Sweetiiih..._