oyah oyah yahh mhmh
Yes of course ndi dziyamikile ndekha,
Kuti ndi ziwoneka chonchi. sizinali zophweka,
Mr.emtee kachikena.
Tickets beats
[chorus]
That's okay
That's alright
Go ahead
Leave life [ x2]
[verse1]
Dziwa dima. umadana ndi Toch,
Pali awili. pamakhala kochi,
Chikond Chikatha. zimakhala chonchi.
Koma may. mukadapola moto,
Pakuti Chikond. Ndi mathelo ankhondo,
ntchimo lili lonse. lili nayo yake mphoto.
Chikond chikatha umadza ndi udan,
Kodi iwe ndine adalakwitsa. Ndan,
Basi tidzawonana may endaniii..
[chorus]
that's okay,
that's alright [ x2]
mr. Patrick ase
[[verse 2]
nzowonad may. pitan,
kwakwana. ndakupililan,
pamaso panga. chokan,
kwinako ndiwona. kut nditan,
Chikond changa chaku.kanikan,
atakhala mwanay,
akakhala nda may,
bas may bye bye
[chorus]
That's okay,
that's alright,
Go ahead,
Leave life,[x2]
[Verse3]
Chikond chanji choyendela season,
Chomangoyambana opanda ma reason,
There is no reason to love,
But it's ok. am so fine,
Yendan may tidza. wonana,
Nzolakwa zathu ozuzika ndi. ana,
Zabodza nzot tinkako. ndana,
Nkhuyu zodya akulu kupota. anaa....
[Chorus]
that's okay,
that's alright,
Go ahead,
leave Life