[Intro]
Ooh Allah, inu wodziwa kudalitsa
[Verse 1]
Dalitsani Sheikh Hussein ndi banja lawo
Mkazi wawo Lucy Abdu Rrasheed ndi mwana wawo Rayhaan Hussein
[Chorus]
Chikondi ndi mtendere zikhale pa pabanja lawo
Ndi maneba onse komanso abwenzi awo
[Verse 2]
Ndipo azilandira chisomo chanu pa banja lawo
Madalitso anu akute banja lawo
Chimwemwe chachikulu chikhale kwa makolo awo
Kuti Akhale mwa mtendere akusowa zisomo zanu
Iwo ndi ochimwa akufunikira chikhululuko chanu
[Chorus]
Chikondi ndi mtendere zikhale pa pabanja lawo
Ndi maneba onse komanso abwenzi awo
[Bridge]
Dzadzani chimwemwe pa banja Hussein inu Rahmaan
Dalitsani mkazi wawo ndi mwana wawo Rayhaan
[Chorus]
Chikondi ndi mtendere zikhale pa pabanja lawo
Ndi maneba onse komanso abwenzi awo
[Outro]
Uchimbichimbi wose ni wenu inu wolemekezeka
kwakwegamira kwewo ni kwamejo jika
komanso akhalitse pa banja lawo
Kufikira tsiku la imfa lawo