Intro
Mmmm
Chorus X4
Chikondi chikamatha,ena mtima umawawa,ena amasangalala,ndimmene zimakhalira
Ena amazipha kumene,ena amalimba mtimaso kumene ndimmene zimakhalira
Vs 1
Mtima sungalephere kuwawa,kudumpha dumpha mtima kuthawa,usiku tulo osabwera,mose wayambila misozi osaphwela
Chorus again X4
Vs2
Ena chikondi chikamatha amasangalala,kutengera ndimmene amakhalira,chikondi chomwechi ena akuzuzika nacho,ena akunenepa nacho inde ndimmene zimakhalira
Chorus again X4
Bridge
Komabe usalire limba mtima,nawe wako uzamupeza tsiku Lina×4