[Intro]
Yeah yeah yeah yeah it's your girl on the beat
Verse1
Mtima wanga uli ndi iwe,
Monga mwezi uli ndi nyenyezi.
Kusakhala ndi iwe, gipa
Ndiwe amene umalitsa moyo wanga
Chorus
Wina walira chonde usazandililitse
Wina walira chonde usazandisiye
Wina walira kuzandisiya zangolira
Wina walira ndimakukonda
Ndimakonda kuposa mpweya wanga.
Ngakhale dziko lonse litakhala chete,
Mtima wanga udzakufuwulira iwe gipa
Iwe gipa
Verse 2
Anzako ayesesa bwera kwaine kundiuza nkhani
Kufuna kutidanitsa
Kma mtima mawanga unakonda iwe
Gipa gipa my love my lov
[Chorus]
Wina walira chonde usazandililitse
Wina walira chonde usazandisiye
Wina walira kuzandisiya zangolira
Wina walira ndimakukonda
[Bridge]
Gipa, ndiwe ameneo unazula mtima
Wanga
[Outro]
Mtima wanga uli ndi iwe, gipa, mpaka mapeto a nthawi
Iwe gipa, iwe gipa