[Verse 1]
Hitler jr Chimwemwe changa chadza m'moyo wanga
Ndikukumbukira nthawi yokoma yomwe idali
[Verse 2]
Ndikuyenda mokondwera ndi mtima wanga
Pakuti njira yodzetsa mtendere ndayipeza
[Chorus]
Chimwemwe changa changonela zanja la yesu
Mtima wanga ukhala wachiyembekezo choona
Pakuti tsopano yesu akulamulila moyo wanga
[Chorus]
Chimwemwe changa chadza
Mtima wanga ukhale wokoma
Ndikusangalala tsopano mwa yesu
[Outro]
Chimwemwe chosatha chimachokela Kwa yesu.