Oooh yeah
Ine ndi jay so
Mbawala ghetto yomwe ija
Yeah yeah
Mavalidwe anga asakupusise
Padeni pagobo sindintchena
Koma kukhala kuzinjoyi
Ndimatchena mwangozi ndiye ndikalowa gobo ambili amati poor man
Kuzangolowa pamusewu ine kutchena mwangozi yeah
Osapusisika ndi validwe
Munthune ndiwakhalidwe
Ndimayenda ndimphavu yamakhalidwe
Yeah yeah
Dollar timasaka no limit
Uzatipeza tigwesa thukuta
Koma pamakhala pa phindu
Munthune ndimasata pa phindu
Ine ndaopa milandu yeah yeah
Sindifuna zoyesana nono yeah yeah
Osapusisika ndi validwe
Munthune ndiwakhalidwe
Ndimayenda ndimphavu yamakhalidwe
Yeah yeah