[Verse 1]
Kulimba mtima mkazi wanga
upitilize kusogolo
sitikhala chochi
mulungu alipo basi
Kulimba mtima kwanu ana anga
mupitilize maso anu pasogolo
limbani mtima basi
tinali ndi zonse za pa moyo
wina wazitenga
chomwe mungadziwe
ndi choti anatipasa
samene watengayo
[Pre-Chorus]
Apa ndili chete
osati ndilibe mau
koma paja osauka
alibe mau
komaso mau anga
kwa mkazi wanga
ndikuuzeni chochi
iyi ndi nkhondo yanga basi
[Chorus]
Limbani mtima basi
Limbani mtima basi
Mulungu alipo basi
Mulungu alipo basi
Limbani mtima basi
mukakhale maso anu pasogolo
Limbani mtima basi
iyi ndi nthawi
[Verse 2]
chifukwa zimene ukuvazi
sizili chocho
inde sitoko kugeni
simalephela komano
iyiyi achita kundionjezela
chifukwa kunali matumba 80
anatuma munthu kuzatengapo 25
akutiso lelo
mkumati kunali matumba 80
zonse ndi nthawi
zonse ndi nthawi
zonse ndi nthawi
[Bridge]
Tinali ndi zonse za pa moyo
wina wazitenga
koma sitigwa pansi
mulungu alipo basi
INE WANU thoko manjomo tengua fayaaa
Apa ndili chete
osati ndilibe mau
koma paja osauka
alibe mau
[Chorus]
Limbani mtima basi
Limbani mtima basi
Mulungu alipo basi
Mulungu alipo basi
Limbani mtima basi
mukakhale maso anu pasogolo
Limbani mtima basi
iyi ndi nthawi.
DJ Dax Six da moz