Oh oh oh oh oh ine ndine batimani m geto sindifoyila ndikamenya veso mafana amafoyila Paine sangafike Iwo ndi ambelela olimbana ndi ine iye abwelela nakuwona mfana uli osageza ndiye Chocho umati ungadise batimani ine ndine mfana oti ndinavaya ndipo khani ya mabebi ndipo ndikulinka ndikamenya vesi ndipo ikuveka ine ndine batimani openga mafana asanje akungo Lila vesi yanga ikulimbana luga faya faya faya nyimbo ndikuimba ndipo zikuveka makape akungosuzumila pa ine sakufika oya oya oya ndikafika pamalo ndipo ndikuchemetsa ndikachoka Palo mafana kumango Lila ine Ndi dada wa ma dada heyi heyi heyi batman batman batman chonde usazafe ukazafa ife tizaku Siwa ndipo tizakulila