feni fenie
uyeeee uuuyeye
mmmm yeeee
(verse)
anayamba ndima Friend's Iwo,,
kumandi uza zaiwe,,
Ndinali ndisanakuonepo,,
Koma kaphekesela kakandipeza,,
Akati kuli ngenge kumusiko
Amadusa aliyese kusuzumilako
Koma lero uli ndi ine.,, Ndineee!!
Umasangalala ndine.,, ndinee!!
(chorus mapiano)
Lero Chimwemwe chasankha Khomo Laine kulira kwako ndimisozi ya inee kuseka kwako ndi Chimwemwe kwaine.
Lero Chimwemwe chasankha Khomo Laine kulira
kwanga ikhare misozi kwaiwe kusenga kwanga chingale Chimwemwe Kwa iwe,,
(Verse)
MMMMMMMMMMMMMH,,
kopanda iwe ndilichabe,,
Mtima wanga lamulira chabe,,
ndiwe Chimwemwe masana ndimazulo,,
kungondisiya uzatenga zambir chabe,,
mmmmmmmmm
Drip katatu