DJ Khai cee my lover beauty nezo chetekela muli iwe but pakati pano wamphwanya mutima wanga nioneka ngati ndine munthu ofuntha cifukwa ca iwe my lover bwelela kumene uli kapena mutima wanga unga bwelelemo cifukwa pano nioneka monga ndine mud man because of you my lover nthawi zonse nezo oneka bwino but cifukwa ca love nioneka mud man