Oh oh oh oh Batman dziko linasitha ndipo chilichose chinasitha ndipo nukudandaula moyo umene ukukhalawu kukamba zona numakuvela chisoni potengela ndimomwe ukuyendela moyo wako ukuwutayilila kwambi koma CHOTI ndikuuze dziko linasitha ndipo chilichose chinasitha ndipo ukuyela kukhala Muthu oziyimila pawekha ndipo Chochobe kukhar Muthu oyima pawekha ndipo ukuyenela kuti ukhale muthu olimba pamachitidye Ako komasotu usayiwale kuti unabadwa wekha ndipo amayi wako ndi azibale wako akamati Ali ndi Muthu wazelu amanena iwe ndipo iweyo ndi amene ungabweletsele chimwemwe pa moyo wawo ndipo chonde usakopeka ndizapadziko lapasi poti zinjoyi sizizatha mpaka kale ndipo Ili ndi dziko ukalitengela udyo limakumaliza iweyo ndiye chonde khala Muthu odekha pa chili chose ndipo ngati ukufuna kuti zako zikhale pa bwino yamba umoyo wa bizinezi iwe pemphelo iva zomwe nukambazi ndipo zigwilitse ntchito umoyo wokhala Nd bizinezi ndi wabwino ndipo chithu chomwe ukufuna chimatheka mosavuta ndipo umalandila ulemu ndipo zitakhala zatsikana zumatheka bwino lomwe akazi omwe ukuwafuna iweyo amakubwelela okha komaso uzidziwa izi Pali mawu oti Oro mtengo ukule bwanji koma sulephela kugwedela thawi zina kholo limatha kisamila m Kono ndukusiya ulibe zochita ndipo umakhala kapolo wa athu Kodi iweyo ukufuna uzakhale paumoyo umenewo chonde chonde vetsela batimani khala Muthu olimbikila poyesa yesa ma bizinezi Kodi iweyo ukufuna kuti ukhale Chochi mpaka kale kumagonela pa ntchito muwathu kumalima vula ikugwa Kodi ukufuna uzingo kulamulidwa zuthu zili zose dziwa kuti naweso ndiwe bwana wa mabwana koma ukayamba kupanga bizinezi iweyo sukuyenela kukhala Muthu ovutika komaso wakula ukuyenela kupeza mkazi wasiliyasi yemwe azathe kusitha moyo wako ndumakupatsa chimwemwe ok tili pa bizinezi tsopano bizinezi sitiyambila ndindalama yochuluka yokha yokha Oro yochepa timayambila BHO BHO ndipo chili chose chimatheka ukudziwa chani umoyo udalila Muthu wina siwabwino olo kuyamba ndipo yambani bizinezi ulendo uno batman