Abdulmalza the bearts, [verse1]ndinanyamuka kupita dziko lá kutali ukoooo ku south Africa kuti ndikapeze thandizo lokhuza banja langa koma zomwe zandichitkila mutu wanga sukugwila [chorus] kulila ndalila mosalekeza ineee!!!!!!! [Verse2] ntchito inali yovuta kukhala movutika ndimapeza ka ndalama kutumiza kuno kumudzi abale angaso nawo andiyenda chá mpeni kundidyela ndalama zanga ndigwila ntengo wanji mwana wamwamuna ine [chorus] tothola mwanawe dziko ndi choncho omwewo abale akowo ndiye dzilombo!!!!!!![verse3] lelo ndabwelako abale omwe mumandipepha thandizo aja ndiwomweso mukuyambitsa kundiseka kundinyoza pamaso pá mzanu Kodi mayi bambo Kodi nkutelo????? [Bridge] mwana wanga dziko ndilimenelo kukhala kwake ndikomweko usafowoke yang'ana patsogolo Pako mtendele ukubwela [final chorus] usade nkhawa moyo uno Palibe wabwino zonse zomwe ukuziwonazi ndichane ukhulupilile mulungu basi zako zizayenda muthu amakhumudwitsa [outro] zitaye pituliza moyo patsogolo thamangitsa maloto ako ukumaniza mwanawe Siwe wekha Ayi zinayamba ndikale, kale, kaleee!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!🎷🎷🎷🎷🎷🎷🎷