[Verse]
Hitler,Ndinali ndi zanga, moyo wanga unali weniweni
Osaziwa kuti sanali dzanga weniweni
Tawona waswa mtima, ooh paja nkhondo ndianasi Ankhoza kukhala ngati dzako koma akumedya khondo chapasi pasi.
[Chorus]
Anali dzanga, tikamayenda kufanana mawanga
Koma alikutali, ndizofuna mtima wanga
Kumbaliku, akuzembelela kadzi wanga
[Verse]
Ndinala ndi, zanga please azanga
Kumasamala ndiyemwe, mukuti ndi zanga
Osaiwala paja nkhondo, ndianasi
Ife
[Chorus]
Zako weniweni amakhala, pamavuto enieni
Sakusiya or, something else change but friend is friend
Kuyenda patsogolo, tikulandira tsogolo