Artist: Newstar Malawi
Song: Title My Beib Girl
I Love you my beib girl, iwe ndamene ndimakonda.
Ndidzatero ndithu mpaka manda, tiziyenda awiri ngati nkhunda.
Kuchoka tsiku lomwe ndinakuona, ndimalephera ngakhale kugona.
Kuchoka pomwe unandilora, nthawi zonse ine ndimakuganizira.
I love you my beib girl, iwe ndamene dzamumveke vero.
Kukhala ndiwe ndimasangalala.
Iwe ndine ndikutali tikafike.
Ndikakuona ndisaname umandiwaza.
Ndingofuna ndizikuona, umandipatsa (patsa).
Muntima mwanga uli ngati nyali.
Ndikulonjeza sidzakusiya, ndidzakukonda mpaka muyaya.
Ndungofuna tizikondana.
Iwe ndine mpaka tsiku (tsiku) lakufa.
Undipatse (patse) chimwemwe.
Ndiwe chikondi changa chamuntima mwanga.
Ndimangofuu (funa) zikuona.
Every day until forever.