[Intro]
Maonekedwe apusisa, mtima wathu uli woyera.
[Verse 1]
Maonekedwe apusisa, koma mtima wathu ndi wachinyengo.
Chikondi ndi mtima osakopeka ndimaonekedwe.
[Chorus]
Mtima ukhoza kukhala wabwino, koma maonekedwe akhope osaoneka bwino?
Chikondi ndi mtima, maonekedwe amatha.
koma mtima uli muyaya?
[Verse 2]
Zinthu za kunja zimasintha, ngati ntchito ya moyo.
Osakonda munthu kamba kamaonekedw.
[Chorus]
Mtima wanga wabwino, ndani angandione Hitler what is love?
Chikondi ndi mtima, zimasintha moyo.
Maonekedwe sizikofunika, ndani weniweni?
Angakonde mkadzi weniweni?
[Outro]
Takondako ife maonekedwe koma osati mtima koma Pano zilipati aah love is liea.song by Jonathan Hitler