Vizasound
Mwai
intro
verse
Ooooh o o oh!!
Uposa msinkhu wanga
Ndili ndi mwai iiii iii ine,
Ofotokoza, zamadalitso angawa.
Chomwe ndinkasowa (ine mwana wanu)
Chinali chikondi chomwe chinali pambali pangapa,
(Kosaka Kwake kunali kutali)
Chifukwa chozi kweza! /
^ mdaliso wangawu unali uli pansi pompo sinafunepo oooo ooh!!
Machitidwe anu ndiwo dabwisa,
Nali ndani osaziwika aaaaaaa
Koma zofuna aaaaaa!!
( ndizo zitalikisa mdaliso waaa inu!!)x4
(Log drum)
Lero ndi chi mdaliso , mwachita baba
inde mwachita nawo moyo wanga.
oooopanda inuyo babaaaaaa
(bwezi ine ndili chabe)
oooooochabe ndekha alone and alone I say !!!!
(choir vocals)
ndinu mwachita ndithu mwachita zazikulu ndiyamika