[Intro]
Ndatopanalo khalidwe lako
[Verse]
Mtima wanga pano unalimba
Khalidwe lako landichosa chikondi changa
Ndichani chomwe sinakuchitile chikondi changa
Chinali chopanda malile
[Chorus]
Khalidwe lako, landipangisa kusitha mtima wanga
Ndikukhulupira iye, sinali nthawi yanga
Mama ine ndaluza nthawi yanga
[Verse]
Mkadzi otani, ongofuna zanthumba mwanga,
basi, apa zathapo, panja zanga wadyapo, koma ugwa ndiye udyapo.
[Chorus]
Khalidwe lako, ladzuzisa ana anthu
Ndikukhulupira iwe, tsopano ndi nthawi
Chikondi chanthu chanthapo
[Outro]
Ndine laho b, lahimu song by Jonathan Hitler