[Intro]
Yeyeyeee aa reyi cee Malawiii aa kanguswa getto music
[Chorus]
Ndimafira iwe (ndimafira iwe baby
Ndichikondi chomwe umandipatsa (ndimafira iwe baby)
Ndichikondi chomwe umandipatsa (ndimafira iwe baby)
[Verse 1]
Hello huny ndayimba phone ndingofuna kupeleka moni ndisaname baby ine ndakusowa ndichikondi chomwe umandipatsa chijaso ndachisowa chonde huny ubweleko kudowa zokhala ndekha zikumabowa
[Verse 2]
Step by step baby tiye tiyende iwe ndi ine tili ndende palibe angandilande baby dzakuthawitsira kutali ine sidzakusiyaso ndikukuuza mtima wanga unatenga ndiwe zanga zonse unatenga ndiwe baby
[Chorus]
Ndimafira iwe (ndimafira iwe baby
Ndichikondi chomwe umandipatsa (ndimafira iwe baby)
Ndichikondi chomwe umandipatsa (ndimafira iwe baby)
[Bridge]
Ndimafira iwe baby (baby
Zoti ndidzakusiya you zokhazo uyiwaleee(uyiwalee yeye
[Outro]
Dzeka boys kampini getto lida empaya