[Intro]
Yeah yeah yeah it's your girl on the beat
Verse 1
Mtima wanga uli ndi iwe,
Monga mwezi uli ndi nyenyezi.
Kusakhala ndi iwe, gipa
Ndiwe amene umalitsa moyo wanga
Chorus
Wina walira chonde usazandililitse
Wina walira chonde usazandisiye
Wina walira kuzandisiya zangolira
Wina walira ndimakukonda
Ndimakonda kuposa mpweya wanga.
Ngakhale dziko lonse litakhala chete,
Mtima wanga udzakufuwulira iwe gipa
Iwe gipa
Verse 2
Anzako ayesesa bwera kwaine kundiuza nkhani
Kufuna kutidanitsa
Kma mtima mawanga unakonda iwe
Gipa gipa my love my love
Iwe amene umalitsa moyo wanga, gipa
Ndikufuna kukhala m’maso ako nthawi zonse
Pre chorus
Gipa, gipa, my love my love
Ndikukonda kuposa mpweya wanga
Ngakhale dziko lonse litakhala chete
Mtima wanga udzakufuwulira iwe gipa
[Verse 2]
Anzako ayesesa bwera, akufuna kundiuza nkhani
Kufuna kutidanitsa, koma mtima unamva iwe
Pang’onopang’ono ndimangokuwona iwe
Gipa, gipa, patali kapena pafupi, ndikumvetsa
[Pre-Chorus]
Wina walira, chonde usazandililitse
Wina walira, chonde usazandisiye
Wina walira kuzandisiya zangolira
Wina walira ndimakukonda
[Chorus]
Gipa, gipa, my love my love
Ndikukonda kuposa mpweya wanga
Ngakhale dziko lonse litakhala chete
Mtima wanga udzakufuwulira iwe gipa
[Bridge]
Iwe ndi ine, mpaka kale
Kumbali ya mavuto, tidzakhala limodzi
Mwa iwe ndipeeza chisomo
Gipa, ndikukuwona mumtsogolo wanga
[Chorus]
Gipa, gipa, my love my love
Ndikukonda kuposa mpweya wanga
Ngakhale dziko lonse litakhala chete
Mtima wanga udzakufuwulira iwe gipa