[Intro]ORT Boy tabesha
Ndikukumbukira chikondi
[Verse 1]
Ndidakukonda iwe kwambiri
Mtima wanga unali wanu
Koma tsopano chikondi chatha
[Chorus]
Chikondi changa sindikundikonda ine
Ndikufuna kudziwa chifukwa
Because they is no love between us anymore , and I don't know why you ka never understand how much I love you
[Verse 2]
Ndikuyang'ana m'maso ako kuti ndione
Koma sindikuwona chiyembekezo
Ndikufuna mayankho
[Chorus]
Chikondi changa sindikundikonda ine
Ndikufuna kudziwa chifukwa
Because they is no love between us anymore, and I don't know why you ka never understand how much I love you
[Chorus]
Chikondi changa sindikundikonda ine
Ndikufuna kudziwa chifukwa
[Outro]
Ndili ndi mtima wokhumba
Zed Zambian music angel beat