Oh oh oh bebi gelo ine ndimakukonda kososa ndipo sindifuna kuti uzidanda ula poti ndiwe yemwe umadzesa chisangalalo chamoyo wanga ndipo sindingakhale popanda iwe poti nditakhala ndi iwe ndimayiwala mavuto omwe ndili nawo pamoyo wanga osanama batimani umandimaliza ndipo sindingakhale popanda iwe batman poti ulingati chili chose chamoyo wanga ndipo or zitavuta maka sindinhakusiye ndipo ndizapanga zokusangalatsa mpaka kale batman batman iwe ndiwe Hilo wanga m nyamata wakwapazani mwana waneleson kapalamula my love