Ndagoma Nanu yesu
Ndagoma Nanu yesu
Ndagoma Nanu yesu
Ndinu fumu yamafuma
Ves 1. *2
Ndani munthu padziko lino
Angafele munthu mzake
Munthu ndani lelolino
Angalolele kutaya moyowu
Vez 2
Koma yesu mwana wamulungu
Musiya ulemelelo
Kudzatifela pamtandapo
Kuwombola moyo wanga
VES 3
Inu yesu mamuna wantanda
Munatsika uko kumwamba
Kunyozedwa m'malo mwa ine
Kuwombola moyo wanga
Ndagoma Nanu yesu
Ndagoma Nanu yesu
Ndagoma Nanu yesu
Ndinu fumu ya mafumu