[Intro]
[Verse 1]
at first tiyamikile inu makolo
potitumiza kusukulu
tikavutika mumatigwira mkono
tikalakwisa ngati asubuhana mumatilangiza
kuti pamawa tizavale oyera mkanda
Oyera mkanda!
mumalola anthu akuny'ozeni chifukwa cha ife
ndi ndani angakwanisenso kutero kuposa inuyo
chachikulu, ndikungomupempha yahwe azikudalisani
[Chorus]
we are happy,..happy!!..happy! today
we are happy,..happy!!..happy! today
tiye ni azanga tisangalale
Koma tikumbukile zammawa
tisangalaleeee!
Koma tikumbukile zapadzana
poti zalerozi zithera pompaaaa
[Verse 2]
yeah! kwa iwe mnzanga
kudekha nkofunika
poti mwa iwe kuzinva ukulu
ako matama kuzionetsela kugulu
kusanvela makolo konse kuli mwa iwe
koma kumbukila komwe tikuchokela
poti tsogolo lako watenga ndiweyo
limbikila role model kwa anthu ena tizakhale...iweeeee!
[Chorus]
we are happy,..happy!!..happy! today
we are happy,..happy!!..happy! today
tiye ni azanga tisangalale
Koma tikumbukile zammawa
(Outro)