Ndimakukonda mwakabisira i hope umadziwa
Ndimachita zonse zoyenera pachikondi dear ma hope
Kukuimbira phone kuphatikiza ma message apa whatsapp
Zonse zija ndipanga kuti udziwe kuti ndimakufuna
Chorus
Ndipatse mpata ndikuonetse kuzuna kwa chikondi changa