[Verse 1]
Mbuye muni menyela kondo ntawi zonse,
Olo siniziba napene niligone
[Chorus]
Mbuye, ndinu chitetezo changa,
Nkhondo zonse mumani menyera,
Usiku na muzuba mumani samalila
[Verse 2]
You sovereign and all powerful ,great and might God you are kulibe wina only you daddy.
Pamene mdima ukufika pa moyo wanga,
Inu mumawala ngati nyali. You are the star that shines so bright Jesus . Yes even I walk through the shadows of death I will fear no evil. You are my good shepherd.
[Bridge]
Nkhondo si yanga, ndi yanu Mbuye, my consuming fire and might man in battle
Ine nima mapemphera, inu mumachita vikulu. the lord is my source of my joy.
[Chorus]
Mbuye, ndinu chitetezo changa,
Nkhondo zonse mumandimenyera,
Usiku na muzuba mumani samalila
I love you Jesus Christ superstar the son of the living God ........