**Artist: Newstar Malawi**
**Song Title: Pa-Iwe**
(Verse 1)
Uli ngati nyenyezi girl,
Uli ngati maluwa beib girl,
Mudziko langa, uli ngati nyali,
Kukhala ndiwe girl, ndimakondwera.
Moyo wanga chilichonse unatenga,
Moyo wanga unakhazikika,
Mwaiwee beib girl,
Ndiwe wekha, umandizura moyo.
(Chorus)
Mtima mwanga ndimafira sangara,
Poti ndiwe unatenga moyo wanga,
Kukhala ndiwe girl, ndimakondwera,
Poti ndiwe unazura moyo wanga.
Ndiwe nkazi okongola,
Palibe wina oposa iwe,
Ndiwe oh- iwe,
Ndiwe my lover.
(Verse 2)
Umandizura moyo ukasekelera,
Umandizura moyo ukamwetulira,
Ndiwe wekha, umandizura moyo,
Ndiwe wekha, ah-ah-ah-ah my love.
Tell me, my lover,
Suzandisiya?
Tandiuuze hee...
Yes, kodi suzandisiya?
(Chorus)
Ndiwe wekha umanditenga moyo,
Ndiwe wekha umandizura moyo,
Ndiwe wekha umanditenga moyo,
Ndiwe wekha umandizura moyo.
Nkazi okongora kuposa aliyese,
Chilichonse ndichokwanira (Pa-iwe),
Ndiwe wekha amene ndimamkonda,
Palibe wina oposa iwe.
(Bridge)
Ntima wanga unakhazikika (Pa-iwe),
Chilichonse ndichokwanira (Pa-iwe),
Chikondi changa chili (Pa-iwe),
Moyo wanga unakhazikika (Pa-iwe).
(Chorus)
Ndiwe wekha umanditenga moyo,
Ndiwe wekha umandizura moyo,
Ndiwe wekha umanditenga moyo,
Ndiwe wekha umandizura moyo.
Nkazi okongora kuposa aliyese,
Chilichonse ndichokwanira (Pa-iwe),
Ndiwe wekha amene ndimamkonda,
Palibe wina oposa iwe.
(Outro)
Ndiwe wekha, umandizura moyo,
Ndiwe wekha, ah-ah-ah-ah my love.
Chikondi changa chili (Pa-iwe),
Moyo wanga unakhazikika (Pa-iwe).