[Intro] this is George Chigome again
[Verse 1]
Ami ndabwera ndi nkhani ya chikondi,
Ndapeza mkazi omanganaye
Banja,zaka zapitazi mwakhalamukufusa,kodi mwana wanga ndiliti uzabwerele,
Kuzandiuza kuti wapeza mkazi,tsiku lija lero Mai lafika, tsiku lilirose iye ndibwenaye, muzamudziwe naye azakudziweni,
[Chorus]
Chimwemwe changa lero ndachipeza, ondisangalasa ine ndilinaye, wapa mtima wanga mulungu wandipasa,
[Verse 2]
Dear tatiye ukawone kumudzi, komwe ukakhale iwe ukadziweko, abale anga iwe akakudziwe, kuti naweso iwo ukawadziwe, asamangonva kut ndapeza mkazi, koma ndimaso awo akakuwone..
[Chorus]
Chimwemwe changa lero ndachipeza, ondisangalasa ine ndilinaye, wapa mtima wanga mulungu wandipasa
[Outro]
This song is dedicated to you my lovely wife I love you so much