[Verse 1]
Ulendo uno okha
ndabwela kuzathokoza
anthu amene ndawaona
kuti ndi azangadi poyamba yamba
arasoni sheko panjema
Komaso mafegi mputhu
Mutoma panjema
Komaso amwene mangolo mumakwana
amoya naceda pa njema
Chiyembekezo pasitolo
Big ben
Alishandiri
[Pre-Chorus]
Inu nose mulungu akudaliseni
Mwapadeladela
mkazi wanga lidia odala
Komanso ana anga witinesi
Daniele
Maiki nanuso
mulungu akusamalileni
Musaiwale
[Chorus]
Panja kuli mulungu
Panja kuli mulungu
Oyamba si inu
Limbani mtima
podikilila mawa
Panja kuli mulungu
Panja kuli mulungu
[Verse 2]
Munali ndi zonse za pa moyo
komano lelo mwasanduka amasiye poyelayela
Musaiwale kumwamba kuli mulungu
Oyamba si inu
Limbani mtima
ngati mtima wanu walira
pali nthawi ya chisomo
pali nthawi ya yankho
[Pre-Chorus]
Inu nose mulungu akudaliseni
Mwapadeladela
mkazi wanga lidia odala
Komanso ana anga witinesi
Daniele
Maiki nanuso
mulungu akusamalileni
Musaiwale
[Chorus]
Panja kuli mulungu
Panja kuli mulungu
Oyamba si inu
Limbani mtima
podikilila mawa
Panja kuli mulungu
Panja kuli mulungu
[Bridge]
kuzacha ndithu
wina azagwada ndimaondo ake
osati ndi mantha
koma ndi choonadi
Lero ululu uli pano
mawa chimwemwe chidzafika
Panja kuli mulungu
ndiwe usiye manja
[Final Chorus]
Panja kuli mulungu
Panja kuli mulungu
Oyamba si inu
Limbani mtima
podikilila mawa
Panja kuli mulungu
Panja kuli mulungu.
DJ DAX SIX DA MOZ