[Intro]
Ooh ooh. Zenizeni mziti.mulungu afuna mziti.tiuzeni zoona kuti tikalowe muumfumu wakumwamba AAA
[Verse 1]
Tizipephela liti..enaakuti km Friday enaso akuti ayi koma Saturday....enaso akuti ayi koma Saturday zenizeni mziti mulungu afunadziti kuti tikalowe muumfumu wakumwamba AAA ooh ooh