[Intro
It's MD again and Aubrey
[Verse]
Usandinamize
Usandibalarise
Ine ndi MD mfana wapa easy
Sindisiya game ndisanayimalize
Ngat ukuyesa ndikunama afuse MA frezo
Amaziwa zambiri kuposa MA hezo
[Chorus]
Zapa easy, zapa easy,ma g ndikut zapa easy, osachulukisa PA kamwa koma inuyo PA easy
[Verse]
Yo yo yo man
Life siyophweka siyapa easy
Ngati ukufuna uzayiphule usazitengere easy
Life siyophweka mphwanga nanga paka kutha mwezi opanda ndalama
Pomwe iwe ukuseweresa ndalama zamakolo ako
Ndikumaziva udada, big man, big boss, bwana wamkulu PA money.
Chosechi ndiwe bwana ogulitsa mapani
[Chorus]
Zapa easy, zapa easy, MA g ndikuti zapa easy, osachulukisa PA kamwa koma inuyo PA easy
[Outro]
Usanyoza poti iwe uli nacho