[Intro]
Oooo!! oooo!
Eeeee eeeeee
Mmmmmm eeee
[Verse 1]
Kodi munatiyiwala?
Pakena tinayambana?
Foni simumatiyimbila
Ngakhele kalata simumatilembela
Kapena simumatiwelengela?
[Chorus]
Zoti munasiya ife, kodi munayiwalila?
Misozi sikata,
Masomu ndimakhumba ndatakuwonani
Kuchoka kwanu kunaswa wathu mtima
Kunasiya chiyembekezo chathu mudima
[Verse 2]
Koma munapita lija mkale kumasano kokadzala chinangwako!!
Komande mwatchonako!!
Chakukomedwetsani tchani kumandako pakena munalemelako
Mesa madzi sayiwala khwawa inu bwanji munatiyiwala
Kungoti makonda abuluziki nde inu munakonda kumeneko
[Chorus]
Zoti munasiya ife, kodi munayiwalila?
Misozi sikatamasomu ndimakumbukira zachanu sichikondi
Koma zowona amayi
Mungatisiye tokha
Mmmmmm mmmmmm