Eh eh eh ai;
Filimoni ase
(Verse 1)
Uwo nzinda wanga
Inu eya wanga wanga,
Kakhomwa uyo!
Koma ndili komkuno
Kumalawi kuno eya komkuno
Apa zaka zikupita, osawonako
Nzinda wakakhomwa
Koma ndili ndichofuna
Mumtima mwanga
Kuzachitira nzinda wanga
Ngati winaso alipo, onga ine,
Mkono m'mwamba ndimudziwe
Kaya ndiwe wamkuno, chakonkuno
Kwathu kuno undiuze;
Ine ndine Filimoni,Kamwachoka
Bambo wanga ndi akamwachoka
Umo mwakakhomwa uwadziwe;
Kaya kwachagunda,kwam'ndola
Kwachikwekwe kapena kwina!
(Chorus)
Eh nzinda wanga uwo
Inu nzinda wanga, kwakakhomwa
Ndikunena zawanga nzinda
Uko kwachagunda;
Eya kwakambwiri, ndiibe mbiri
(Verse 2)
Nthawi ikubwera
Nzinda wanga uzakondwa,
Koma enabe azandida
Popanda chowalakwira
Ndizakhala m'dani wayena
Ndizakhala m'dalitso kwayena;
Poti anthu ali mwawanthu
Ena sazakondwa pondiwona
Poti Ali abwezi ake asatana
Izi zili kwatonse, osati ndimose
(Chorus)
Akamwachoka, Ali ndimoyo
Ali ndimwana, eh Filimoni
Uyu ndigolide, inde waife tose;
Nzinda wake ndiuno
Eh uno wakakhomwa
Kwawo ndikuno, eh mudzamuona
Kakhomwa T.C ase
Nzinda wanga uwo!
Kamwa K ase;
Mws