[Intro]
[Verse 1]
Filimoni ase,
Eh eh eh ai
Ndineyo wanu
Ticheze monga ine nzanu
Kaya simundiva,
Koma ine ndinena
Pano ndapeza wanga
Eh Inu namwari
Iyeyu ndi happiness
Inde happiness yaine
Abale nose mudziwe
Azanga nose mundive
Ine ndakumana naye
Uyu ndi happiness
Inu happiness yaine
[Chorus]
Uyu ndimbambande
Ndipo ndindende
Mulungu adayankha
[Verse 2]
Iwe happiness
Eh eh tavetsera
Iwe happiness
Tsono tavetsera
Ine ndine Filimoni
Osati chako chisoni
Eh monga sergeant
Ine nzakutetezera
Or chitsotso m'maso mwako
Ai sichizagwera
Ndati monga sergeant
Nzakuveka nyota
Ulemu mchimake
Monga mama sergeant
[Chorus]
Tsogolo lathu tikoze
Tisazakhale makoswe,
Iwe happiness
Eh eh eh ai
You're my happiness
Now and again
With me sergeant K
[Bridge]
Kamwa k ase!!
[Outro]