[Intro]
Usiku wopanda mtendere
[Verse 1]
Penapake amunafe timazuzidwa
Ndi akazi wa timakanidwa
Mkazi yu amandikana
Nthawi zambiri kumufusila
Amanditukwana
Koma lero wandiuza kuti ndi iyankha mawa
Ndine kupita pa den kukanika kugona
Kumangoona kuchedwa kucha
[Chorus]
Kunja kunjaaaah
Kukuchedwa kucha
Kukuchedwa kucha
Kunja kunjaaaah
Kukuchedwa kucha
Kukuchedwa kucha
[Verse 2]
Kuyesa umu ndi umu tulo osabwela
Kumwa ma pills ogonesa
Komabe tulo osabwela
I try and try but no more
Bola akandiuza answer
Zikanakhala Better
Ndikanapeza mpumulo
Aleast Ndikanapeza tulo
[Chorus]
Kunja kunjaaaah
Kukuchedwa kucha
Kukuchedwa kucha
Kunja kunjaaaah
Kukuchedwa kucha
Kukuchedwa kucha
[Outro]
Ndikufuna tulo, kupumura kwa mtendere