[Intro]
Jenzo yeah
Yeah, uh...
[Verse 1]
Ine ndi ma braq, tili tight ngati chain,
Timakweza game, osadya pain,
Tili ndi dream, si za nthawi ya ma fake,
M’tauni yonse amadziwa tikabwera — earthquake!
Ma opanga hate, tima’passa basi,
BNG timayenda monga classic,
Palibe kusowa, palibe panic,
Tikakhala pa mic, energy — automatic.
[Chorus]
BNG forever, we rise and conquer,
Tima’fight limodzi, stronger as one,
Braq Nigaz Gang — number one contender!