(chorus)
Mesa munandisiya mkati sinditha kuvepa
Ndine chizoba umkati sundimvetsa
Unandipatsa dzina loti sindikalimvetsa
Ukandiona pena kumandizemba
(ves)
Phone yanga osayimba palibepo mission
Ndine shasha nde, ndimayendela mission
Ndinakuuza osandisiya ndikupanga mission
Koma sunandimvele poti unalibeso vision
Pano ukubwera basi kufuna kundiyesa
Ndalama ndinapezazi basi ufuna kundidyela
(chorus)
Mesa munandisiya mkati sinditha kuvepa
Ndine chizoba umkati sundimvetsa
Unandipatsa dzina loti sindikalimvetsa
Ukandiona pena kumandizemba
(ves)
Phone yanga osayimba palibepo mission
Ndine shasha nde, ndimayendela mission
Phone yanga osayimba palibepo mission
Ndine shasha nde, ndimayendela mission
(chorus)
Mesa munandisiya mkati sinditha kuvepa
Ndine chizoba umkati sundimvetsa
Unandipatsa dzina loti sindikalimvetsa
Ukandiona pena kumandizemba