kulira kwa mtima
Verse 1
Ndimakukonda, ndimakupatsa zonse zanga
Koma ukundiona ngati ndili chabe
Ukandifuna ndi pomwe umandikumbukira
Chikondi chizikomo osati kuwawa
Verse 2
Ndimayesasa kma sindikukwanira
Nthawi zonse ndili pano, koma sukundiona
Lero ndazindikira mtengo wanga
Munthu amene umamukonda
Ndiamene sakukonda
Verse 3
Kuseka kwanga ndi kwa iwe, misozi nayonso ndi yako
Koma iwe ukungonditenga ngati chizolowezi
Ndimafuna mwamuna, osati munthu wongodutsa
Ndikhale wako kapena ndipite