[Intro]
I miss you dear
I miss you. Not in some cheesy “Let’s hold hands and be together forever kind of way”. I just miss you, plain and simple. I miss your presence in my life. I miss you always being there for me. I miss you best friend.
[Verse 1]
I miss you dear, I need you
Mukupita kwathawi tinayiwalana
Zoti thawi zonse tinkasamalana
Tinali limodzi pakulila
Mezi ulindala kutiwalila
Awa ndimasiku osatheka kuwayiwalila
Inali thawi yokoma ndi kayiganizila
All days are nights to see till I see thee, And nights bright days when dreams do show thee to me.
[Chorus]
I miss you
[Verse 2]
Poti thawi mkachitsilu
Usiku umenewo sudzabwelaso
Koma ndimadziva ngati mbali yanga ine inafa
Ndipo thawi inandilanda chithu chachikulu moyo mwanga
[Chorus]
I miss you dear,
I keep myself busy with the things I do but every time I pause, I still think of you.
Koma ndawasowa masiku amwene timkagona limodzi
Pomwe tinkatetezana muzovuta
Zoti unali chishango changa lelo ngati bodza
[Outro]
Tinotasangana munguva yakakodzera
When I miss you, sometimes I listen to music or look at pictures of you, not to remind me of you but to make me feel as if I'm with you. It makes me forget the distance and capture you.