Ndine nfana OGEZA mboni yanga ndi SPONGE
Ndine nfana OWALA bestie wanga ndi TORCH
Ndimakapewa ti BANana… NTCHOCHI yeah
(make space for the ace)
HOOK:
Ndahasa ndasanja lero ndili BHO
Kwacha yapezeka ndili mma WIN'KO
Ukauze kamfana kakumwa WIN'KO
Kut ndimadana ndi zopusa ine ndi WINIKO
Verse 1:
Mamuna wako ndi zoba monga anzako saku KHAFA?
Akakanga NAMAZA ndekut siakudya BAFA
Ikwetu unagwidwa ndi kape alibe BRAINS nkomwe
Amayenda wapas alibe BENZ nkomwe
Zaine mwayenera kuSIMBA
Nditsegula ma SHOP inu mukutsegula MMIMBA
Ndili mma WIN'ko ife si aNZANUTU
Ndima vera mkamwa ndimadana ndi zaNKUTU
...