[Intro]
Gipa, gipa my love
[Verse 1]
Mtima wanga uli ndi iwe, monga mwezi ndi nyenyezi
Kusakhala ndi iwe, gipa, ndiwe amene umalitsa moyo wanga
Chorus
Wina walira chonde usazandililitse, wina walira chonde usazandisiye
Wina walira kuzandisiya zangolira, wina walira ndimakukonda
Verse 2
Ngakhale dziko lonse litakhala chete, mtima wanga udzakufuwulira iwe gipa
Iwe gipa, gipa my love
[Verse 2]
Anzako ayesesa bwera kwaine kundiuza nkhani
Kufuna kutidanitsa, koma mtima mawanga unakonda iwe
Gipa gipa my love my love
[Bridge]
Ndikuona mtima ukugona, kuwukira mu mtima wanga choncho
Khalani chete, palibe chosadziwika
[Chorus]
Ngakhale dziko lonse litakhala chete, mtima wanga udzakufuwulira iwe gipa
Iwe gipa, gipa my love
[Outro]
Gipa, gipa, my love, nthawi zonse
Ine ndikukonda, mtima wanga ndani anandidzudzula