[Verse 1]
Poyamba ndithokoze Mlungu pondipatsa moyo kufika tsikuli
I know simphavu zanga olo nzeru zanga
Ichi ndichisomo Yhawe wamphavu zonse
Mutalenga zonse nalenganso munthu
Chikondi chake abale chodabwitsa
Though I walk through the valley of the shadow of death
I will fear no evil I know You are with me
Ndinena mau awa molimbi ntima
Pozindikila kuti
In your arms, there I am safe
Ndinu nokha mbuye
[Chorus]
Ndinu nokha mbuye (eeehhhh)
Munandilenga muchifanizo chanu
Ndinu nokha Yesu (mmmmh)
Munandiyeletsa ndi mwazi wanu
Ndinu nokha Tate (yeaaa)
Munandimasula kunsinga zasatana
Nandipatula kudziko lamazunzo
Ndinu nokha mbuye
[Verse 2]
Ngakhale ndiyenda dziko lanjala, nthenda mavuto
Ndimadziwabe (I know) ndili ndi Mbuye
Amandikonda kosalekeza
Ndidzamtamanda kosalekeza
Ali chomwecho dzulo, dzana lero
Adzakhalabe kunthawi zonse
You who never change (no, no, no)
No you Never sleep nor do you tire
Landirani ulemu
(ndinu nokha mbuye)
[Chorus]
[Bridge]
Mantha ndilibe (heh)
Ndinu njira kumapazi anga
Simulekera pompo
Muyala gome, right before my enemies
In the presence of my enemies, you raise me higher (higher and higher)
Muyenda nane
Opanda manyazi ndiyimba
Opandanso mantha ndiyenda
Coz I know
You reign, you reign, you reign!
Yhawe you reign
(Ndinu nokha)
[Chorus]