It's Newstar Malawi Again
Uli ngati nyenyezi girl
Uli ngati maluwa beib girl
Mudziko langa uli ngati nyali, kukhala ndiwe girl ndimakondwera
Moyo wanga chilichonse unatenga
Moyo wanga unakhazikikaa
mwaiwee beib girl
Ndiwe wekha umandizura moyo
Mtima mwanga ndimafira sangara
Poti ndiwe unatenga moyo wanga
Kukhala ndiwe girl ndimakondwera
Poti ndiwe unazura moyo wanga
Ndiwe nkazi okongora
Palibe wina oposa iwe
Ndiwe oh- iwe
Ndiwe my lover
Umandizura moyo ukasekelera
Umandizura moyo ukamwetulira
Ndiwe wekha umandizura moyo
Ndiwe wekha ah-ah-ah-ah my love
Tell me, my lover
Suzandisiya?
Tandiuuze hee....
Yes, kodi suzandisiya?
Ndiwe wekha umanditenga moyo
Ndiwe wekha umandizura moyo
Ndiwe wekha umanditenga moyo
Ndiwe wekha umandizura moyo
Nkazi okongora kuposa aliyese
Chilichonse ndichokwanira (Pa-iwe)
Ndiwe wekha amene ndimamkonda
Palibe wina oposa iwe
Ntima wanga unakhazikika (Pa-iwe)
Chilichonse ndichokwanira (Pa-iwe)
Chikondi changa chili (Pa-iwe)
Moyo wanga unakhazikika (Pa-iwe)