(INTRO)
-Nadisi Btm Bayo Ak Amutho(hear dis)
(CHORUS)
-baibe yaine
-ndimafila ayiree
-yokongola
-nkazi wamakhalidwee
-baibe yaine
-ndimafila ayiree
-yokongola
-nkazi wamakhalidwee
(VERSE 1)
-Nadis btm bayo ak Thomson maluwa
-mi love you
- i care
-beib girl for sure
-ndiwe okongola makhalidwe
-nkazi umandimaliza
-ndiwe wekha wapamtima
-please osasintha.
-ndiwe waine babie
-chilichonse zakupatsaa
-ndikadwala nkazi ndiwe makhwala
-babie kwako ndikuwalaa.
(CHORUS)
-baibe yaine
-ndimafila ayiree
-yokongola
nkazi wamakhalidwee
-baibe yaine
-ndimafila ayiree
-yokongola
-nkazi wamakhalidwee
(VERSE 2)
-babe girl ndiwe waine machine gun
-tikakhala limodzi
-umandipangitsa kukhala Handsome
-maka maka ukamanditchula thomsom
-woman Na pretty
-fashion with beauty
-mi love you
-take it easy
(CHORUS)
-baibe yaine
-ndimafila ayiree
-yokongola
nkazi wamakhalidwee
-baibe yaine
-ndimafila ayiree
-yokongola
nkazi wamakhalidwee